Mu mau ake odyeredwa ndalama yo yemwe dzina lake ndi Mada iye wati;👇
"Adha awawa ndine tinali paubwenz. mkat mwandime ndimafuna ndigule katundu winawake. I had 250k nde sinampeze katundu. Gee anandiuza kut akagule kushop kwanzake he will top up. Sinanga boyfriend nnampatsa ndalama ija kenaka zii. That was February. Anazandiuza zaprogram inayake and zimafunika kut ndipereke 150k. I sent the money. Anandiuza kwao kuli maliro afuna atumize ndalama koma ili ku bank so he is tied up with work sangakatenge ndalama. I sent 45k. Anandiuza ndimubwereke mini cooker I borrowed him. Nnauzidwa kut wapanga ngozi wapindika nthiti and Ali ku zomba central. Mmalumikizana nd sister wake. Nnauzidwa ntumize 15k. I sent. On all these counts kwao sinnakafikeko ndimaletsedwa. Only to learn even nkhan yangoziyo amanama. Anabwereka 165k from my friend without my knowledge. Then the friend anayamba kundikwenya ine. Ku police amangowaimba nyimbo. Ndafotokoza in brief and u are allowed to call me names coz mmapanga zinthu mosaganizira koma pamapeto tilire limodz. Those who know me akudziwa kut ndalama zimenezo kut nzipeze ineyo nmagobola size kukana"- anatsindika motero kwinaku akusisina
Ase kabweze ndalama chonde tsoka ukuliyambalo ase🙌
Related News
EIGHT MZUZU WARDS HAVE BEEN LEFT HOMELESS AFTER THEIR HOUSES COLLAPSED DUE TO PERSISTENT RAINFALL.
May 15, 2025
According to the report reaching our desk, Nsongwe, Saulsberry Line, Masasa, Chibavi, Zolozolo, Chip...
GABADINHO MHANGO ASUMILA TIMU YAKE ITAGWILITSA NTCHITO CHITHUNZI CHAKE MOSAENERA.