NYASALAND MUZIK WORLD

NYASALAND MUZIK WORLD

GABADINHO MHANGO ASUMILA TIMU YAKE ITAGWILITSA NTCHITO CHITHUNZI CHAKE MOSAENERA.

Published on: May 15, 2025
News Image

Gabadinho Mhango akufuna alipidwe ndalama zokwana R828,000, zomwe zili pafupifupi K82.8 miliyoni timu yomwe amasewera ku sasafilika yotchedwa Marumo Gallants itagwilitsa ntchito chithunzi chake mosaenera. Malingana ndi malipoti Gabadinho watengera ku khoti timu yakeyi atavutana pa nkhani yi kotero mlandu wu ukuenera kumvedwa mu khoti lalikuru ku Johannesburg.